Judges 18:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono anthu a fuko la Dani aja adapita, ndipo pamene Mika adaona kuti anthuwo ngamphamvu kupambana iyeyo, adangobwerera kunyumba kwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nayenda ulendo wao ana a Dani; ndipo Mika pakuona kuti anamposa mphamvu, anatembenuka nabwerera kunyumba kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho anthu a fuko la Dani anapitiriza ulendo wawo. Mika ataona kuti anthuwo anali amphamvu kuposa iye, anangotembenuka kubwerera kwawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nayenda ulendo wao ana a Dani; ndipo Mika pakuona kuti anamposa mphamvu, anatembenuka nabwerera kunyumba kwace.