Judges 18:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ali kunyumba kumeneko, adazindikira liwu la mnyamata wachilevi uja ndipo adapita kwa iye nakamufunsa kuti, “Udabwera ndi yani kuno? Ukuchita chiyani kuno? Ukugwira ntchito yanji kuno?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pokhala iwo m'nyumba ya Mika, anazindikira mau a mnyamata Mleviyo, napatukirako, nanena naye, Anadza nawe kuno ndani? Uchitanji muno? Ukhala nacho chiyani kuno?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ali ku nyumba ya Mika anazindikira mawu a mnyamata, Mlevi uja. Choncho anapita kwa iye namufunsa kuti, “Unabwera ndi ndani kuno? Nanga ukuchita chiyani ku malo ano? Komanso nʼchifukwa chiyani uli kuno?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pokhala iwo m'nyumba ya Mika, anazindikira mau a mnyamata Mleviyo, napambukirako, nanena naye, Anadza nawe kuno ndani? ucitanji muno? ukhala naco ciani kuno?