Judges 18:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero anthu a fuko la Dani aja ankapembedza fano lija limene Mika adapanga, nthaŵi yonse pamene chihema cha Mulungu chinali ku Silo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Motero anadziikira fano losema la Mika, limene adalipanga, masiku onse okhala nyumba ya Mulungu ku Silo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho anthu a fuko la Dani ankapembedza fano limene Mika anapanga nthawi yonse pamene nyumba ya Mulungu inali ku Silo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Motero anadziikira fane losema la Mika, limene adalipanga, masiku onse okhala nyumba ya Mulungu ku Silo.