Judges 18:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iyeyo adaŵauza kuti, “Ndili pa chipangano ndi Mika, adandilemba ntchito ndipo ndine wansembe wake.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ananena nao, Mika anandichitira chakutichakuti, napangana nane za ntchito, ndipo ndikhala wansembe wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anawawuza zimene Mika anamuchitira ndipo anati, “Iye anandilemba ntchito ndipo ndine wansembe wake.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ananena nao, Mika anandicitira cakuti cakuti, napangana nane za nchito, ndipo ndikhala wansembe wace.