Judges 18:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo aja adamuuza kuti, “Chonde, tatifunsirako kwa Mulungu, kuti tidziŵe ngati ulendo wathu uno tiyende bwino.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo ananena naye, Utifunsire kwa Mulungu, kuti tidziwe ngati ulendo wathu timukawo udzakoma.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka iwo anati kwa iye, “Chonde tifunsire kwa Mulungu kuti tidziwe ngati ulendo wathuwu tiyende bwino.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo ananena naye, Utifunsire kwa Mulungu, kuti tidziwe ngati ulendo wathu timukawo udzakoma.