Judges 19:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene ankayandikira ku Yebusi, nkuti kuli madzulo ndithu, ndipo mtumiki uja adauza mbuyake kuti, “Bwanji tsopano tingopatuka, kuloŵa mu mzinda wa Ayebusiwu ndi kukagona momwemo?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pofika iwo pa Yebusi linalimkulowa dzuwa, ndi mnyamata anati kwa mbuye wake, Tiyeni, tipatukire mudzi uwu wa Ayebusi ndi kugona pomwepa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akuyandikira ku Yebusi nʼkuti kutada ndithu. Tsono mtumiki uja anawuza mbuye wake kuti, “Tiyeni, tipatukire ku mzinda wa Ayebusiwa ndipo tigone.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pofika iwo pa Yebusi linalimkulowa dzuwa, ndi mnyamata anati kwa mbuye wace, Tiyeni, tipambukire mudzi uwu wa Ayebusi ndi kugona pomwepa.