Judges 19:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mbuyake adayankha kuti, “Sitipatuka kuloŵa mu mzinda wa alendo amene sali Aisraele. Koma tipitirira mpaka ku Gibea.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mbuye wake ananena naye, Tisapatukire mudzi wachilendo, wosati wa ana a Israele, koma tipitirire kunka ku Gibea.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mbuye wake anamuyankha kuti, “Ayi, tisapatukire ku mzinda wa alendo, anthu amene sali Aisraeli. Koma tipitirire mpaka ku Gibeya.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mbuye wace ananena naye, Tisapambukire mudzi wacilendo, wosati wa ana a lsrayeli, koma tipitirire kumka ku Gibeya,