Judges 19:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero adauza mtumiki wakeyo kuti, “Tiye tikafike pafupi ndi malo ndatchulawo, ndipo tikagone ku Gibea kapena ku Rama.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati kwa mnyamata wake, Tiyeni, tiyandikire kwinako: tigone m'Gibea, kapena m'Rama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono anamuwuza mtumiki wake uja kuti, “Tiye tipite ku amodzi a malo awa, ku Gibeya kapena ku Rama ndipo tikagone kumeneko.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati kwa mnyamata wace, Tiyeni, tiyandikire kwinako: tigone m'Gibeya, kapena m'Rama.