Judges 19:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho adapitirira nayenda ulendo wao, ndipo dzuŵa lidaŵaloŵera atafika pafupi ndi Gibea, mzinda wa fuko la Benjamini.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Napitirira iwo, nayenda, ndi dzuwa linawalowera pafupi pa Gibea, ndiwo wa Benjamini.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho nayenda ulendo wawo, ndipo dzuwa linawalowera akuyandikira ku Gibeya mʼdziko la Benjamini.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Napitiriraiwo, nayenda, ndi dzuwa linawalowera pafupi pa Gibeya, ndiwo wa Benjamini.