Judges 19:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho adapita nawo kunyumba kwake, naŵapatsa chakudya abulu aja. Ndipo alendowo adasamba mapazi ao, nalandira chakudya ndi chakumwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo anamlonga m'nyumba yake, napatsa abulu chakudya; ndipo iwo anasamba mapazi ao, nadya, namwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho anapita nawo ku nyumba yake, ndipo anawapatsa abulu ake chakudya. Alendo aja anasamba mapazi awo, nalandira chakudya ndi chakumwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo anamlonga m'nyumba yace, napatsa aburu cakudya; ndipo iwo anasamba mapazi ao, nadya, namwa.