Judges 19:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo m'maŵa kulikucha, mkaziyo adabwera nagwa pansi pakhomo pa nyumba ya munthu uja m'mene munali mwamuna wake muja. Adakhala pamenepo ali thasa mpaka kudayera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nadza mkaziyo, kutacha, nagwa pakhomo pa nyumba ya munthu padali mbuye wake, kufikira kutayera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo mmawa kukucha mzikazi uja anabwerera nakagwa pansi pa khomo pa nyumba imene mwamuna wake anali, ndipo anakhala pomwepo mpaka kunayera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nadza mkaziyo kutaca, nagwa pakhomo pa nyumba ya munthu padali mbuye wace, kufikira kutayera.