Judges 19:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mpongozi wakeyo, bambo wake wa mkazi uja, adamuuza kuti aswere, choncho adakhalako masiku atatu. Ankadya, namamwa ndi kumagona kumeneko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mpongozi wake, ndiye atate wa mkaziyo, anamuimika kuti akhale naye masiku atatu; nadya namwa nagona komweko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mpongozi wake, yemwe anali abambo a mtsikanayo, anamupempha kuti aswere. Choncho anakhalako masiku atatu. Ankadya, kumwa ndi kugona komweko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mpongozi wace, ndiye atate wa mkaziyo, anamuimika kuti akhale naye masiku atatu; nadya namwa nagona komweko.