Judges 19:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene munthuyo adanyamuka kuti azipita, mpongozi wake adamkakamiza kuti agonenso komweko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo munthuyo ananyamuka kuti amuke; koma mpongozi wakeyo anamkakamiza, nagonanso komweko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo pamene mwamunayo anakonzeka kuti azipita, apongozi ake anamuwumirizanso kuti asapite. Choncho anagona komweko usiku umenewo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo munthuyo ananyamuka kuti amuke; koma mpongozi waceyo anamkakamiza, nagonanso komweko.