Judges 2:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mbadwo wonsewo udafa. Tsono padauka mbadwo wina pambuyo pake umene sudadziŵe Chauta kapenanso ntchito zija Chauta adaachitira Aisraelezi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiponso mbadwo uwu wonse unasonkhanidwa kuikidwa kwa makolo ao; nuuka mbadwo wina pambuyo pao; wosadziwa Yehova kapena ntchitoyi adaichitira Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼbado onse utapita kukakhala ndi anthu a mtundu awo, kenaka panauka mʼbado wina umene sunadziwe Yehova ngakhale ntchito zazikulu zimene Yehova anachitira Aisraeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiponso mbadwo uwu wonse unasonkhanidwa kuikidwa kwa makolo ao; nuuka mbadwo wina pambuyo pao; wosadziwa Yehova kapena nchitoyi adaicitira Israyeli,