Judges 2:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuyambira tsopano sindidzapirikitsanso mtundu wina uliwonse umene Yoswa adasiya pamene ankamwalira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inenso sindionjeza kuingitsa pamaso pao a mitundu ina imene Yoswa adaisiya pakufa iyeyu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inenso sindidzapirikitsanso mtundu uli wonse wa anthu amene Yoswa anawasiya pomwalira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
lnenso sindionjeza kuingitsa pamaso pao a mitundu yina imene Yoswa adaisiya pakufa iyeyu;