Judges 2:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero ndidzaŵayesa Aisraele kuti ndiwone ngati adzasamala zoyenda m'njira ya Ine Chauta, monga adachitira makolo ao, kapena ai.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti ndiyese nayo Israele ngati adzasunga njira ya Yehova kuyendamo monga anaisunga makolo ao, kapena iai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzatero kuti ndiwayese Aisraeli ndi kuona ngati adzasamala kuyenda mʼnjira ya Ine Yehova monga momwe ankachitira makolo awo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti ndiyese nayo Israyeli ngati adzasunga njira ya Yehova kuyendamo monga anaisunga makolo ao, kapena iai.