Judges 2:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene mngelo wa Chauta adalankhula mau ameneŵa kwa Aisraele onse, anthuwo adayamba kufuula ndi kulira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, pamene mthenga wa Yehova ananena mau awa kwa ana onse a Israele, anthuwo anakweza mau ao, nalira misozi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mngelo wa Mulungu atayankhula izi kwa Aisraeli, onse analira mokweza,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, pamene mthenga wa Yehova ananena mau awa kwa ana onse a Israyeli, anthuwo anakweza mau ao, nalira misozi.