Judges 2:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yoswa atauza anthu kuti apite, Aisraele adapita aliyense ku dera la choloŵa chake, kuti akhazikike konko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene Yoswa atawalola anthu amuke, ana a Israele anamuka, yense ku cholowa chake, dziko likhale laolao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yoswa atawuza Aisraeli kuti achoke, iwo anapita kukatenga dzikolo, aliyense dera lake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene Yoswa atawalola anthu amuke, ana a Israyeli anamuka, yense ku colowa cace, dziko likhale lao lao.