Judges 2:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yoswa, mwana wa Nuni, mtumiki wa Chauta, adamwalira ali ndi zaka 110.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yoswa mwana wa Nuni, mtumiki wa Yehova anafa wa zaka zake zana ndi khumi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yoswa mwana wa Nuni, mtumiki wa Yehova, anamwalira ali ndi zaka 110.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yoswa mwana wa Nuni, mtumiki wa Yehova anafa wa zaka zace zana ndi khumi.