Judges 20:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Aisraele onse adasonkhana atagwirizana chimodzi pofuna kulimbana nawo mzindawo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero amuna onse a Israele anasonkhanira mudziwo, olunzika ngati munthu mmodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho anthu a ku Israeli anasonkhana pamodzi nagwirizana chimodzi, kukalimbana ndi mzindawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero amuna onse a Israyeli anasonkhanira mudziwo, olunzika ngati munthu mmodzi.