Judges 20:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mafuko a Aisraele adatuma anthu kwa fuko lonse la Benjamini, kuti akafunse kuti, “Kodi zoipa zimene mwachita pakati panupazi nzotani?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mafuko a Israele anatuma anthu mwa fuko lonse la Benjamini, ndi kuti, Choipa chanji ichi chinachitika mwa inu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mafuko a Israeli anatumiza anthu kwa fuko lonse la Benjamini kukafunsa kuti, “Kodi zoyipa zachitika pakati panuzi ndi zotani?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mapfuko a Israyeli anatuma anthu mwa pfuko lonse la Benjamini, ndi kuti, Coipa canji ici cinacitika mwa inu?