Judges 20:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho Abenjamini onse adatuluka m'mizinda yao ku Gibea kukamenyana nkhondo ndi Aisraele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ana a Benjamini anasonkhana kuchokera kumidzi kunka ku Gibea, kuti atuluke kulimbana ndi ana a Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼmalo mwake, Abenjaminiwo anatuluka mʼmizinda yawo ku Gibeya kukamenyana ndi Aisraeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ana a Benjamini anasonkhana kucokera ku midzi kumka ku Gibeya, kuti aturuke kulimbana ndi ana a Israyeli.