Judges 20:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku limenelo Abenjamini adasonkhanitsa ankhondo 26,000, osaŵerenga anthu ena a ku Gibea 700 osankhidwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anawerenga ana a Benjamini a m'midzi tsiku lija amuna zikwi makumi awiri mphambu zisanu ndi chimodzi akusolola lupanga; osawerenga okhala m'Gibea, ndiwo amuna osankhika mazana asanu ndi awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku limenelo Abenjamini anasonkhanitsa kuchokera ku mizinda yawo ankhondo 26,000 amalupanga awo, osawerengera anthu ena 700 a ku Gibeya amene anasankhidwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anawerenga ana a Benjamini a m'midzi tsiku lija amuna zikwi makumi awiri mphambu zisanu ndi cimodzi akusolola lupanga; osawerenga okhala m'Gibeya, ndiwo amuna osankhika mazana asanu ndi awiri.