Judges 20:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwa anthu onseŵa panali anthu 700 amanzere, amene ankatha kulasa ndi mwala ngakhale tsitsi limodzi, osaphonya konse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwa anthu awa onse munali amuna osankhika mazana asanu ndi awiri amanzere, yense wa iwo amaponya mwala mwa maluli osaphonya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwa onsewa panali ankhondo 70 amanzere amene aliyense anali wodziwa kulasa ngakhale tsitsi limodzi ndi mwala osaphonya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwa anthu awa onse munali amuna osankhika mazana asanu ndi awiri amanzere, yense wa iwo amaponya mwala mwa maluli osaphonya.