Judges 20:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nawonso Abenjamini adatuluka ku Gibea ndipo tsiku limenelo adapha Aisraele 22,000.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo ana a Benjamini anatuluka m'Gibea, naononga a Israele tsiku lija zikwi makumi awiri mphambu ziwiri, kuwagoneka pansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
A fuko la Benjamini anatuluka ku Gibeya ndipo tsiku limenelo anapha Aisraeli 22,000 ku nkhondoko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo ana a Benjamini anaturuka m'Gibeya, naononga a Israyeli tsiku lija zikwi makumi awiri mphambu ziwiri, kuwagoneka pansi,