Judges 20:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Aisraelewo adalimbitsana mtima ndipo adakhazika ankhondo ao kachiŵiri pa malo omwe aja pamene adaaŵakhazika tsiku loyamba lija.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anthu, ndiwo amuna a Israele, anadzilimbitsa nanikanso nkhondo kumene anandandalika tsiku loyambalo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ankhondo a Israeli analimbikitsananso mtima ndipo anasonkhanitsanso kachiwiri ankhondo awo pa malo pamene anawandandalika poyamba paja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anthu, ndiwo amuna a Israyeli, anadzilimbitsa nanikanso nkhondo kumene anandandalika tsiku loyambalo.