Judges 20:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho Aisraele adafika pafupi, kuti akalimbane ndi Abenjamini tsiku lachiŵiri lake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero ana a Israele anayandikira ana a Benjamini m'mawa mwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Aisraeli anayandikiranso pafupi ndi fuko la Benjamini tsiku lachiwiri lake kuti amenyane nawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero ana a Israyeli anayandikira ana a Benjamini m'mawa mwace.