Judges 20:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'menemo nkuti anthu a fuko la Benjamini atamva kuti Aisraele apita ku Mizipa. Tsono Aisraele adati, “Tiwuze, kodi zoipa zoterezi zachitika bwanji?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ana a Benjamini anamva kuti ana a Israele adakwera kunka ku Mizipa. Nati ana a Israele, Nenani, choipa ichi chinachitika bwanji?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu a fuko la Benjamini anali atamva kuti Aisraeli apita ku Mizipa. Tsono Aisraeli anati, “Tiwuzeni, zinthu zoyipa izi zinachitika bwanji.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ana a Benjamini anamva kuti ana a Israyeli adakwera kumka ku Mizipa, Nati ana a Israyeli, Nenani, coipa ici cinacitika bwanji?