Judges 20:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapita kukamenyana ndi Abenjamini tsiku lachitatu lake, nakhazika ankhondo ao kuti athire nkhondo mzinda wa Gibea monga masiku ena aja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ana a Israele anakwerera ana a Benjamini tsiku lachitatu, nanika pa Gibea monga nthawi zina.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku lachitatu anapita kukamenyana ndi Benjamini ndipo anayika ankhondo mʼmalo mwawo kuti amenyane ndi Gibeya monga anachitira poyamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ana a Israyeli anakwerera ana a Benjamini tsiku lacitatu, na nika pa Gibeya monga nthawi zina.