Judges 20:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adati, “Taŵapirikitsa monga poyamba paja.” Koma Aisraele adati, “Tiyeni tithaŵe kuti apite ku miseu chapatali ndithu ndi mzinda wao.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ana a Benjamini anati, Tawakantha pamaso pathu monga poyamba paja. Koma ana a Israele anati, Tithawe, tiwakokere kutali ndi mudzi kumakwalala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abenjamini ankanena kuti, “Tikuwagonjetsa monga poyamba.” Koma Aisraeli ankanena kuti, “Tiyeni tithawe kuti apite ku msewu chapatali ndi mzinda wawo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ana a Benjamini anati, Tawakantha pamaso pathu monga poyamba paja. Koma ana a Israyeli anati, Tithawe, tiwakokere kutari ndi mudzi kumakwalala.