Judges 20:38 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono chizindikiro chimene adaapangana Aisraele a gulu lalikulu ndi anthu obisalira aja chinali chakuti, akafukiza utsi wambiri ngati mtambo mumzindamo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma kunali chizindikiro choikika pakati pa amuna a Israele ndi olalirawo, ndicho chakuti afukitse mtambo wa utsi kumudzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chizindikiro chimene Aisraeli anapangana ndi anthu obisalira aja chinali chakuti obisalira aja akangofukiza utsi wambiri ngati mtambo mu mzindamo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma kunali cizindikilo coikika pakati pa amuna a Israyeli ndi olalirawo, ndico cakuti afukitse mtambo wa utsi kumudzi.