Judges 20:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Mlevi uja, mwamuna wa mkazi wophedwayo, adati, “Ndidafika ku Gibea, mzinda wa Abenjamini, ineyo ndi mzikazi wanga, kuti tigone kumeneko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mlevi, mwamuna wa mkazi anaphedwayo, anayankha nati, Ndinadza ine ku Gibea wa Benjamini, ine ndi mkazi wanga wamng'ono, kugonako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Mlevi uja, mwamuna wa mkazi wophedwa uja anayankha nati, “Ine ndinapita ku Gibeya mʼdziko la Benjamini pamodzi ndi mzikazi wanga kuti tikagone kumeneko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mlevi, mwamuna wa mkazi anaphedwayo, anayankha nati, Ndinadza ine ku Gibeya wa Benjamini, ine ndi mkazi wanga wamng'ono, kugonako.