Judges 20:41 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pomwepo Aisraele adabwerera ndipo Abenjamini adayamba kuwopa ndi kutaya mtima, pakuti adaaona kuti zoopsa zili pafupi kuŵagwera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Natembenuka amuna a Israele; nadabwa amuna a Benjamini; popeza anaona kuti chidawagwera choipa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Aisraeli anabwerera ndipo Abenjamini anachita mantha, chifukwa anaona kuti zoopsa zili pafupi kuwagwera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Natembenuka amuna a Israyeli; nadabwa amuna a Benjamini; popeza anaona kuti cidawagwera coipa.