Judges 20:42 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake Abenjamini adayamba kuthaŵa Aisraelewo, naloŵa njira ya ku dondo. Koma nkhondo idaŵapeza, ndipo adaphedwa ndi Aisraele amene ankatuluka mu mzinda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nabwerera iwo pamaso pa amuna a Israele kunka njira ya chipululu; koma nkhondo inawalondetsa; ndi aja otuluka m'mudzi anawaononga pakati pao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho anathawa pamaso pa Aisraeli kudzera njira ya ku chipululu, koma nkhondo inawapeza. Ndipo anaphedwa kumeneko ndi Aisraeli amene anachokera mu mzindamo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nabwerera iwo pamaso pa amuna a Israyeli kumka njira ya cipululu; koma nkhondo inawaloodetsa; ndi aja oturuka m'mudzi anawaononga pakati pao.