Judges 20:44 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Abenjamini amene adaphedwa analipo 18,000. Onsewo anali anthu olimba mtima kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo adagwa a Benjamini amuna zikwi khumi ndi zisanu ndi zitatu; iwo onse ndiwo ngwazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abenjamini 18,000 olimba mtima anaphedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo adagwa a Benjamini amuna zikwi khumi ndi zisanu ndi zitatu; iwo onse ndiwo ngwazi.