Judges 20:47 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthu 600 okha adakafika ku dondo ku thanthwe la Rimoni, nakakhala ku thanthwe la Rimoniko miyezi inai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma amuna mazana asanu ndi limodzi anabwerera nathawira kuchipululu, ku thanthwe la Rimoni, nakhala m'thanthwe la Rimoni miyezi inai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma anthu 700 anabwerera ndi kuthawira ku chipululu ku thanthwe la Rimoni kumene anakhalako miyezi inayi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma amuna mazana asanu ndi limodzi anabwerera nathawira kucipululu, ku thanthwe la Rimoni, nakhala m'thanthwe la Rimoni miyezi inai.