Judges 20:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidamtenga mzikaziyo ndi kumduladula nthulinthuli, nkuzitumiza kwa fuko lililonse la Aisraele. Ndithudi anthu amene aja achita zinthu zonyansa ndi zoipa kwabasi m'dziko lino la Israele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo ndinagwira mkazi wanga wamng'ono ndi kumgawa ndi kumtumiza m'dziko lonse la cholowa cha Israele, pakuti anachita chochititsa manyazi ndi chopusa m'Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndinatenga mzikazi wangayo ndi kumudula nthulinthuli ndikuzitumiza kwa fuko lililonse la Aisraeli. Anthu amenewa, zedi achita chinthu chonyansa kwambiri mʼdziko lino la Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo ndinagwira mkazi wanga wamng'ono ndi kumgawa ndi kumtumiza m'dziko lonse la colowa ca Israyeli, pakuti anacita cocititsa manyazi ndi copusa m'lsrayeli.