Judges 20:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu onse adadzuka pamodzi nati, “Palibe munthu ndi mmodzi yemwe mwa ife amene apite ku hema lake, palibe amene abwerere kunyumba kwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anthu onse anauka ngati munthu mmodzi, ndi kuti, Palibe mmodzi wa ife adzamuka kuhema kwake, kapena kupatukira nyumba yake,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu onse anayimirira ngati munthu mmodzi nanena kuti, “Palibe mmodzi wa ife amene apite ku nyumba kwake. Palibe amene abwerere ku nyumba kwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anthu onse anauka ngati munthu mmodzi, ndi kuti, Palibe mmodzi wa ife adzamuka kuhema kwace, kapena kupambukira nyumba yace,