Judges 20:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma tsono zimene tiŵachite anthu a ku Gibea ndi izi: tipita kukalimbana nawo mzindawo potsata zimene maere atiwuze.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma tsopano ichi ndicho tidzachitira Gibea: tidzaukwerera ndi kulota maere.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma tsopano chimene ife tichite ndi dziko la Gibeya ndi ichi: Tidzapita kukamenyana nawo potsatira zimene maere anene.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma tsopano ici ndico tidzacitira Gibeya: tidzaukwerera ndi kulota maere.