Judges 21:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwowo adati, “Nkofunika kuti anthu otsalira a fuko la Benjamini akhale nazo zidzukulu, kuti fuko lao lisafafanizike pa mtundu wa Israele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati iwo, Pakhale cholowa cha iwo opulumuka a Benjamini, lingafafanizidwe fuko m'Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anati, “Abenjamini amene anapulumukawa ayenera kukhala ndi zidzukulu, kuti mtundu wa Israeli usafafanizike.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati iwo, Pakhale colowa ca iwo opulumuka a Benjamini, lingafafanizidwe pfuko m'Israyeli.