Judges 21:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe sitingathe kuŵapatsa ana athu aakazi kuti aŵakwatire.” Paja Aisraele anali atalumbira kuti, “Akhale wotembereredwa munthu amene apatse Mbenjamini mkazi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma sitikhoza ife kuwapatsa ana athu akazi akhale akazi ao; pakuti ana a Israele adalumbira ndi kuti, Atembereredwe wakupatsa Abenjamini mkazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ife sitingathe kuwapatsa ana anthu aakazi kuti akwatire. Paja tinalumbira kuti, ‘Akhale wotembereredwa aliyense amene adzapereka mwana wake wamkazi kwa mwamuna wa fuko la Benjamini kuti akwatire.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma sitikhoza ife kuwapatsa ana athu akazi akhale akazi ao; pakuti ana a Israyeli adalumbira ndi kuti, Atembereredwe wakupatsa Abenjamini mkazi.