Judges 21:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Aisraele adamvera chifundo abale ao a fuko la Benjamini nati, “Fuko limodzi lachotsedwa m'dziko la Israele lero lino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ana a Israele anamva chifundo chifukwa cha Benjamini mbale wao, nati, Fuko limodzi lalikhidwa pa Israele leroli.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Aisraeli anamva chisoni chifukwa cha abale awo, Abenjamini. Iwo anati, “Lero fuko limodzi lachotsedwa mu Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ana a Israyeli anamva cifundo cifukwa ca Benjamini mbale wao, nati, Pfuko limodzi lalikhidwa pa Israyeli leroli.