Judges 21:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti m'mene anthu ankasonkhana, adangoona kuti palibe munthu ndi mmodzi yemwe wa ku Yabesi-Giliyadi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti pamene anawerenga anthu, taonani, panalibe mmodzi komweko wa okhala m'Yabesi-Giliyadi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene anthu anawerengana anangoona kuti anthu a ku Yabesi Giliyadi palibe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti pamene anawerenga anthu, taonani, panalibe mmodzi komweko wa okhala m'Yabesi-gileadi,