Judges 3:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Chauta adasiya mitundu ina ya anthu, kuti ayese nayo Aisraele, ndiye kuti Aisraele onse amene sadamenye nao nkhondo ku Kanani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iyo ndiyo mitundu ya anthu anaisiyapo Yehova kuyesa nayo Israele, ndiwo onse amene sanadziwe nkhondo zonse za Kanani;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iyi ndi mitundu ya anthu yomwe Yehova anayisiya kuti ayese nayo Aisraeli amene sanadziwe kumenya nkhondo mu Kanaani
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iyo ndiyo mitundu ya anthu anaisiyapo Yehova kuyesa nayo Israyeli, ndiwo onse amene sanadziwa nkhondo zonse za Kanani;