Judges 3:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero dziko lidakhala pa mtendere zaka makumi anai. Pambuyo pake Otiniyele, mwana wa Kenazi, adamwalira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo dziko linapumula zaka makumi anai; ndi Otiniyele mwana wa Kenazi anafa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo mʼdzikomo munakhala mtendere zaka makumi anayi. Kenaka Otanieli mwana wa Kenazi anamwalira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo dziko linapumula zaka makumi anai; ndi Otiniveli mwana wa Kenazi anafa.