Judges 3:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapita kukapereka msonkho kwa Egiloni, mfumu ya ku Mowabu, amene anali wonenepa kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapereka mtulo kwa Egiloni, mfumu ya Mowabu; koma Egiloni ndiye munthu wonenepa ndithu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anakapereka msonkho kwa Egiloni, mfumu ya Mowabu, amene anali munthu wonenepa kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapereka mtulo kwa Egiloni, mfumu ya Moabu; koma Egiloni ndiye munthu wonenepa ndithu.