Judges 3:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta ankangofuna kuti mibadwo yonse ya Aisraele idziŵe kumenya nkhondo, ndiponso kuti aphunzitse makamaka amene sadaidziŵe nkhondo nkale lonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chifukwa chake ndicho chokha chakuti adziwitse mibadwo ya ana a Israele ndi kuwaphunzitsa nkhondo, ngakhale iwo okhaokha osaidziwa konse kale;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
(Yehova anachita izi kuti Aisraeli onse aphunzire kumenya nkhondo; makamaka amene nʼkale lonse sanadziwe kumenya nkhondo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
cifukwa cace ndico cokha cakuti adziwitse mibadwo ya ana a Israyeli ndi kuwaphunzitsa nkhondo, ngakhale iwo okha okha osaidziwa konse kale;