Judges 3:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Ehudi ndi dzanja lake lamanzere, adasolola lupanga pa ntchafu yake yakumanja ndi kubaya nalo mfumuyo pa mimba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Ehudi anatulutsa dzanja lake lamanzere nagwira lupanga ku ntchafu ya kulamanja nampyoza m'mimba mwake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ehudi ndi dzanja lake lamanzere, anasolola lupanga pa ntchafu yake ya kumanja ndi kubaya nalo mfumuyo pa mimba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Ehudi anaturutsa dzanja lace lamanzere nagwira lupanga ku ncafu ya kulamanja nampyoza m'mimba mwace;