Judges 3:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ehudi atachoka, atumiki a mfumu adabwera. Ataona kuti zitseko za chipinda cham'mwamba nzokhoma, adaganiza kuti, “Kapena mfumu ikudzithandiza m'katimo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo atatuluka iye, anadza akapolo ake; napenya, ndipo taonani pamakomo pa chipinda chosanja mpofungulira; nati iwo, Angophimba mapazi m'chipinda chake chosanja chopitidwa mphepo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ehudi atachoka, atumiki a mfumu aja anabwera, ndipo ataona kuti zitseko za chipinda chapamwamba zinali zokhoma anaganiza kuti mwina mfumu ikudzithandiza mʼkatimo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ataturuka iye, anadza aka polo ace; napenya, ndipo taonani pamakomo pa cipinda cosanja mpofungulira; nati iwo, Angophimba mapazi m'cipinda cace cosanja copitidwa mphepo.