Judges 3:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ehudi adathaŵa pamene iwo ankachedwa nkudikira. Adapitirira malo a miyala yozokota ija, nathaŵira ku Seira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Ehudi anapulumuka pakuchedwa iwo, napitirira pa mafano osema, napulumuka kufikira Seira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ehudi anathawa pamene iwo ankadikira. Iye anadzera ku malo a miyala yozokotedwa kuja ndi kuthawa kupita ku Seiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Ehudi anapulumuka pakucedwa iwo, napitirira pa mafano osema, napulumuka kufikira Seira.